JavaScript isn't enabled in your browser, so this file can't be opened. Enable and reload.
EYA! Start up Challenge and Incubation Programme
Do you have an agribusiness idea, or are struggling to get your agribusiness to grow? If yes, Luanar Agribiz Hub and Synergy, invites you to apply for an exciting opportunity to prove that U can do it, by enrolling into a Start Up Challenge and Agribusiness Incubation programme. Fill the following form to apply.
Kodi uli ndi chiganizo choyambitsa kapena kukulitsa bizinesi ya ulimi? Ngati yankho lako lili EYA! A LUANAR Agribiz Hub ndi Synergy akukonzerani mpikisano wotchedwa EYA! Start up challenge kuti uwonetse kuti ndi zotheka. Yankhani mafunso otsatilawa kuti mulowe nawo mu mpikisanowu komanso mu pologalamu ya maphunziro a bizinesi ya ulimi (Agribusiness Incubation)
Sign in to Google
to save your progress.
Learn more
* Indicates required question
Full name? Dzina Lanu?
*
Your answer
National ID? Nambala ya chaunzika?
*
Your answer
Sex? Jenda?
*
Male/Mamuna
Female/Nkazi
Age? Zaka zanu?
*
Your answer
Phone number/Nambala yanu yafoni?
*
Your answer
Email address? Imelo adilesi?
Your answer
Physical address? Malo amene mukukhala?
*
Your answer
Are you applying alone or as lead member of a group? Mukulembera nokha kapena ngati gulu?
*
Alone/Ndekha
Group/Gulu
If in a group, List members of your group, gender and national ID numbers? Ngati muli gulu, Lembani mayina anthu a gulu lanu, jenda lawo ndi nambala ya chaunzika yawo?
Example; Name of Member/Female/VZN792 Mwachitsanzo; Dzina la membara/jenda/VZN792
Your answer
Indicate your business stage of development? Nenani siteji ya bizinesi yanu?
*
Idea/Maganizo
Early stage/Kumayambiliro kwa bizinesi
If idea – Describe your product? Ngati ali maganizo, fotokozani maganizo abizinesi yanu?
Your answer
If idea – what is your target market and marketing strategy? Ngati ali maganizo, fotokozani kuti muzigulitsa kwa ndani ndi njira zowagulitsira kwa makasitomara anu?
Your answer
If idea – where will the business be located? Ngati ali maganizo, fotokozani kumene muzapangire buzinesi yanu?
Your answer
If idea – have you done anything so far to get started? Ngati ndi malingaliro chabe, fotokozani zimene mwapangako zothandizira ku bizinesi yanu iyambike?
Your answer
If early stage – name of business? Ngati muli gawo lachiyambi labizinesi yanu, lembani dzina la bizinesi yanu?
Your answer
If early stage – Type of the business? Ngati muli gawo lachiyambi labizinesi yanu, ndi bizinesi ya mtundu wanji?
Sole proprietor/Buzinesi yanokha
Partnership/M'gwirizano wabizinesi
Cooperative/Bizinesi ya m'gwirazano
Limited company/Kampani yocheperako
Clear selection
If early stage –When was it established and number of full time paid employees including owner? Ngati muli gawo lachiyambi labizinesi yanu, buzinesi yanu inakhazikitsidwa litilo ndi namabala ya anthu amene munawalemba ntchito ndi nambala?
Your answer
If early stage – Your market and competitor? Ngati muli gawo lachiyambi labizinesi yanu, Fotokozani nsika wanu ndi amene mukupikisana nawo pa bizinesi?
Your answer
What support are you seeking to reach your entrepreneurial goals? Mukusaka chithandizo chanji pa bizinesi yanu?
*
Your answer
Does your business/ idea solve any social challenges in your area? If yes Explain how Kodi bizinesi yanu ikuthandiza kuthetsa nawo m'gwirizano wa anthu amudera lanu? Fotokozani ngati zili choncho?
*
Your answer
What motivated you to apply for this programme? Chakulimbikitsani kuti mulembere nawo mwayi umenewu?
*
Your answer
Submit
Clear form
Never submit passwords through Google Forms.
This form was created inside of LUANAR, Bunda College Campus.
Report Abuse
Forms